The Jaki Show

Ku USA, mtsikana uyu, Aubrey Vanlandingham, wa dzaka 17 akuzengedwa mulandu wochita nkhaza kwa zinyama.

Aubrey ali ndi mbuzi imene amayipanga train kuti idzipanga ma trick. Kumanvera ndikupanga zimene yauzidwa.

Eni mbuziwa, amalowa mipikisano ya mbuzi. Amene mbuzi yake ikuchita bwino, amapambana nkumalandira mphoto.

Mbuzi ya Aubrey imangolephera, pamene mbuzi ya mzake, yomwe anayipatsa dzina loti Willy the goat 🐐, imangowina.

Willy the Goat 🐐 anangopezeka atafa mwadzidzidzi. Achipatala atamuyeza, anapeza kuti Willy anadyetsedwa poison.

Atayang'ana ma CCTV, anawona Aubrey atalowa mu khola la Mbuziyo nkuibayira injection mkamwa.

Anayang'ana search history ya phone ya Aubrey, anapeza kuti amafusa gugo kuti pakufunika poison kwambiri bwanji kuti uphe chinyama.

Aubrey wavomera mulanduwu.

Sidenote
🐐

#Nkhani

1 month ago | [YT] | 84



@LouisAndrew-jr1yj

Eee kom nkhani zakenso πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

4 weeks ago | 0

@TracyMundira

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚ aaaa ndiwo ngt zimenezo kumaziseweresa

1 month ago | 0

@stephenkbanda598

Kkkk nsanje ndichilomboπŸ˜€

1 month ago | 0

@TachikoMwanamanga

Side note The Goat 🐐the queen πŸ«… πŸ˜‚

1 month ago | 0

@PheliaKbmwamboh

Komatu maiko enawo ngobhowanso mlandu wanyama ndiye kuulondoloza wamunthu kuukhalira ndichinyengo, nawonso awaaaaaa nsanje ndimbuzi mpaka

1 month ago | 0

@emmanuelkapsyphiri

Angoseweretsa ndiwo anthuwa

1 month ago | 1

@AmakaBAbie

Zaziiii koma zina ukamva

1 month ago | 0

@FloraBanda-w7t

Kkkkkk

1 month ago | 0

@tinashemarley

Zina umangoona waziputa

1 month ago | 0