The Jaki Show
Ku USA, mtsikana uyu, Aubrey Vanlandingham, wa dzaka 17 akuzengedwa mulandu wochita nkhaza kwa zinyama.Aubrey ali ndi mbuzi imene amayipanga train kuti idzipanga ma trick. Kumanvera ndikupanga zimene yauzidwa.Eni mbuziwa, amalowa mipikisano ya mbuzi. Amene mbuzi yake ikuchita bwino, amapambana nkumalandira mphoto.Mbuzi ya Aubrey imangolephera, pamene mbuzi ya mzake, yomwe anayipatsa dzina loti Willy the goat 🐐, imangowina.Willy the Goat 🐐 anangopezeka atafa mwadzidzidzi. Achipatala atamuyeza, anapeza kuti Willy anadyetsedwa poison.Atayang'ana ma CCTV, anawona Aubrey atalowa mu khola la Mbuziyo nkuibayira injection mkamwa.Anayang'ana search history ya phone ya Aubrey, anapeza kuti amafusa gugo kuti pakufunika poison kwambiri bwanji kuti uphe chinyama.Aubrey wavomera mulanduwu.Sidenote 🐐 #Nkhani
3 weeks ago | [YT] | 83
The Jaki Show
Ku USA, mtsikana uyu, Aubrey Vanlandingham, wa dzaka 17 akuzengedwa mulandu wochita nkhaza kwa zinyama.
Aubrey ali ndi mbuzi imene amayipanga train kuti idzipanga ma trick. Kumanvera ndikupanga zimene yauzidwa.
Eni mbuziwa, amalowa mipikisano ya mbuzi. Amene mbuzi yake ikuchita bwino, amapambana nkumalandira mphoto.
Mbuzi ya Aubrey imangolephera, pamene mbuzi ya mzake, yomwe anayipatsa dzina loti Willy the goat 🐐, imangowina.
Willy the Goat 🐐 anangopezeka atafa mwadzidzidzi. Achipatala atamuyeza, anapeza kuti Willy anadyetsedwa poison.
Atayang'ana ma CCTV, anawona Aubrey atalowa mu khola la Mbuziyo nkuibayira injection mkamwa.
Anayang'ana search history ya phone ya Aubrey, anapeza kuti amafusa gugo kuti pakufunika poison kwambiri bwanji kuti uphe chinyama.
Aubrey wavomera mulanduwu.
Sidenote
🐐
#Nkhani
3 weeks ago | [YT] | 83