The Jaki Show

A University of Oxford mogwirizana ndi ma researchers ena atatsimikiza za kupezeka kwa Super earth.

Super earth ndi planet imene inayiwona dzaka ziwiri zapitazo ndipo akhala akufufuza zambiri.

New super earth, ndiyayikulu x 6 dziko lapansi. Anayipatsa dzina lokuti HD 20794.
Akuti super earth simazungulira dzuwa lathuli koma nyenyezi ina yangati dzuwalo.

Distance yake kuchoka kwathu kuno ndi 20 light years.

Akatswiri akukhulupilira kuti uku anthu akhoza kukhalako bwinobwino nde akufufuzako.

Sidenote
20 light years mu dzaka zathu ndi 186,282 years

#Nkhani

2 weeks ago | [YT] | 112



@Lizzie-h1k

Mmmm...kkkkk 20 light year...yachuluka...kulibe amene angadzakafikeko...kkkkk

1 week ago | 0

@YamikanAlexander

Best jaki

1 week ago | 0

@hannahmoses480

Nde mayendwe azakhala bwanji kuti tikafike kumeneko Ofunika kupanga machawi tikagwile Malo abwinotu 🤣🤣🤣 rent yatikwana kuno

1 week ago | 0

@KateChiumia

Chimene amafuna agalu amenewa(scientist) azachipeza hmmm 🙌

1 week ago | 1

@wysonnamaona6497

Wautari komko. Kukadzala mbatata ndi mtedza basi

1 week ago | 0

@mphatsomataya1498

Moni moni

1 week ago | 0

@stephenkbanda598

Ndiye zaka zonsezo ndizotheka anthu kukafikako amoyo?

1 week ago | 0

@InnocentMaluwa-qj1qn

❤️

1 week ago | 0

@HellenKanyemba

Tisamukire kumeneko mwina zinthu nzotchipa

1 week ago | 0

@PearsonSalima

Tachulukanadi muno sakani planet Ina🙄

1 week ago | 0

@Ntatesibusisombata

Kodi iwe ukutichani

1 week ago | 0

@lawrencekuzomba7350

"The Tower of babel" ideology

2 weeks ago | 0

@ChikoMasapula

These are just fictions theories... Ntchito Zama atheist izi asayansi bodza

1 week ago | 0