A University of Oxford mogwirizana ndi ma researchers ena atatsimikiza za kupezeka kwa Super earth.
Super earth ndi planet imene inayiwona dzaka ziwiri zapitazo ndipo akhala akufufuza zambiri.
New super earth, ndiyayikulu x 6 dziko lapansi. Anayipatsa dzina lokuti HD 20794. Akuti super earth simazungulira dzuwa lathuli koma nyenyezi ina yangati dzuwalo.
Distance yake kuchoka kwathu kuno ndi 20 light years.
Akatswiri akukhulupilira kuti uku anthu akhoza kukhalako bwinobwino nde akufufuzako.
Sidenote 20 light years mu dzaka zathu ndi 186,282 years
The Jaki Show
A University of Oxford mogwirizana ndi ma researchers ena atatsimikiza za kupezeka kwa Super earth.
Super earth ndi planet imene inayiwona dzaka ziwiri zapitazo ndipo akhala akufufuza zambiri.
New super earth, ndiyayikulu x 6 dziko lapansi. Anayipatsa dzina lokuti HD 20794.
Akuti super earth simazungulira dzuwa lathuli koma nyenyezi ina yangati dzuwalo.
Distance yake kuchoka kwathu kuno ndi 20 light years.
Akatswiri akukhulupilira kuti uku anthu akhoza kukhalako bwinobwino nde akufufuzako.
Sidenote
20 light years mu dzaka zathu ndi 186,282 years
#Nkhani
1 week ago | [YT] | 111